Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 18:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kodi pali chosatheka ndi Yehova?+ Pa nthawi yoikidwiratu ndidzabweranso kwa iwe chaka chamawa. Ndidzabweranso nthawi ngati yomwe ino, ndipo Sara adzakhala ndi mwana wamwamuna.”

  • Yeremiya 32:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Kalanga ine! Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+ Inuyo ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu yanu+ ndi dzanja lanu lotambasula.+ Nkhaniyi si yovuta kwa inu.+

  • Zekariya 8:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Ngakhale kuti m’masiku amenewo otsalira a anthu awa adzaona kuti zimenezo n’zosatheka, kodi zidzakhalanso zosatheka kwa ine?’+ watero Yehova wa makamu.”

  • Maliko 14:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Kenako anati: “Abba,* Atate,+ zinthu zonse n’zotheka kwa inu. Ndichotsereni kapu iyi. Komatu osati mwa kufuna kwanga, koma mwa kufuna kwanu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena