Genesis 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi pali chosatheka ndi Yehova?+ Pa nthawi yoikidwiratu ndidzabweranso kwa iwe chaka chamawa. Ndidzabweranso nthawi ngati yomwe ino, ndipo Sara adzakhala ndi mwana wamwamuna.” Yobu 42:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndadziwa kuti inu mumatha kuchita zinthu zonse,+Ndipo palibe zimene simungakwanitse.+ Yeremiya 32:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Kalanga ine! Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+ Inuyo ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu yanu+ ndi dzanja lanu lotambasula.+ Nkhaniyi si yovuta kwa inu.+ Zekariya 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Ngakhale kuti m’masiku amenewo otsalira a anthu awa adzaona kuti zimenezo n’zosatheka, kodi zidzakhalanso zosatheka kwa ine?’+ watero Yehova wa makamu.” Luka 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iye anawauza kuti: “Zinthu zosatheka ndi anthu n’zotheka ndi Mulungu.”+
14 Kodi pali chosatheka ndi Yehova?+ Pa nthawi yoikidwiratu ndidzabweranso kwa iwe chaka chamawa. Ndidzabweranso nthawi ngati yomwe ino, ndipo Sara adzakhala ndi mwana wamwamuna.”
17 “Kalanga ine! Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+ Inuyo ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu yanu+ ndi dzanja lanu lotambasula.+ Nkhaniyi si yovuta kwa inu.+
6 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Ngakhale kuti m’masiku amenewo otsalira a anthu awa adzaona kuti zimenezo n’zosatheka, kodi zidzakhalanso zosatheka kwa ine?’+ watero Yehova wa makamu.”