Zekariya 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Ine ndipulumutsa anthu anga kuchokera kudziko lakumʼmawa ndiponso lakumadzulo.+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:7 Nsanja ya Olonda,1/1/1996, tsa. 17
7 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Ine ndipulumutsa anthu anga kuchokera kudziko lakumʼmawa ndiponso lakumadzulo.+