Zekariya 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mʼnyumba ya Yuda mudzatuluka mtsogoleri.Mudzatulukanso wolamulira wothandiza,Komanso mudzatuluka uta womenyera nkhondo.Woyangʼanira* aliyense adzatuluka mwa iye. Onse adzatulukira limodzi.
4 Mʼnyumba ya Yuda mudzatuluka mtsogoleri.Mudzatulukanso wolamulira wothandiza,Komanso mudzatuluka uta womenyera nkhondo.Woyangʼanira* aliyense adzatuluka mwa iye. Onse adzatulukira limodzi.