Zekariya 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 M’nyumba ya Yuda mudzatuluka mtsogoleri.+ Mudzatulukanso wolamulira ndi wothandiza,+ komanso mudzatuluka uta womenyera nkhondo.+ Kapitawo aliyense adzatuluka mwa iye.+ Anthu onsewa adzatuluka mwa iye.
4 M’nyumba ya Yuda mudzatuluka mtsogoleri.+ Mudzatulukanso wolamulira ndi wothandiza,+ komanso mudzatuluka uta womenyera nkhondo.+ Kapitawo aliyense adzatuluka mwa iye.+ Anthu onsewa adzatuluka mwa iye.