Genesis 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+ Ezara 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano kwa nthawi yochepa, Yehova Mulungu wathu watikomera mtima+ mwa kutisiyira anthu opulumuka,+ ndiponso mwa kutipatsa malo otetezeka* m’malo ake oyera kuti maso athu awale,+ inu Mulungu wathu, ndi kutitsitsimutsa pang’ono mu ukapolo wathu.+
10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+
8 Tsopano kwa nthawi yochepa, Yehova Mulungu wathu watikomera mtima+ mwa kutisiyira anthu opulumuka,+ ndiponso mwa kutipatsa malo otetezeka* m’malo ake oyera kuti maso athu awale,+ inu Mulungu wathu, ndi kutitsitsimutsa pang’ono mu ukapolo wathu.+