15 Komabe pali ena amene sanachite zimenezi chifukwa ali ndi mzimu woyera wa Mulungu. Iwo akufuna kukhala ndi ana amene angakhaledi anthu a Mulungu. Choncho samalani kuti mukhale ndi maganizo oyenera ndipo musachitire zachinyengo akazi anu amene munawakwatira muli anyamata.