-
Malaki 2:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Komabe pakati panu pali ena amene atsimikiza mtima kuti asachite zoterezi. Iwo akufuna kukhala ndi ana amene angakhaledi anthu a Mulungu.*+ Mphamvu ya Mulungu ikutsogolera anthu amenewa pa zonse zimene akuchita. Tsopano inunso ganizirani mofatsa ndipo mukhale ndi maganizo oyenera.+ Tsimikizani mtima kuti musachitire zachinyengo akazi anu amene munawakwatira muli anyamata.+
-