Malaki 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa ine ndimadana ndi zoti anthu azithetsa mabanja,”+ watero Yehova Mulungu wa Isiraeli. “Ndimadana ndi munthu wankhanza.* Samalani kuti mukhale ndi maganizo oyenera ndipo musamachite zachinyengo,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. Malaki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:16 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 42 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2018, tsa. 11 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2016, tsa. 11 Galamukani!,6/2015, tsa. 135/8/1999, tsa. 112/8/1994, ptsa. 29-30 Nsanja ya Olonda,10/1/2013, tsa. 95/1/2002, ptsa. 17-186/15/1987, tsa. 11 Tsiku la Yehova, ptsa. 121-122, 126-128
16 Chifukwa ine ndimadana ndi zoti anthu azithetsa mabanja,”+ watero Yehova Mulungu wa Isiraeli. “Ndimadana ndi munthu wankhanza.* Samalani kuti mukhale ndi maganizo oyenera ndipo musamachite zachinyengo,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
2:16 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 42 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2018, tsa. 11 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2016, tsa. 11 Galamukani!,6/2015, tsa. 135/8/1999, tsa. 112/8/1994, ptsa. 29-30 Nsanja ya Olonda,10/1/2013, tsa. 95/1/2002, ptsa. 17-186/15/1987, tsa. 11 Tsiku la Yehova, ptsa. 121-122, 126-128