Malaki 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Inu mwatopetsa Yehova ndi mawu anu.+ Koma mukunena kuti, ‘Tamutopetsa bwanji?’ Ponena kuti, ‘Aliyense wochita zoipa ndi wabwino kwa Yehova ndipo amasangalala naye,’+ kapena ponena kuti, ‘Kodi Mulungu wachilungamo ali kuti?’” Malaki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:17 Nsanja ya Olonda,5/1/2002, tsa. 188/1/1998, tsa. 6
17 “Inu mwatopetsa Yehova ndi mawu anu.+ Koma mukunena kuti, ‘Tamutopetsa bwanji?’ Ponena kuti, ‘Aliyense wochita zoipa ndi wabwino kwa Yehova ndipo amasangalala naye,’+ kapena ponena kuti, ‘Kodi Mulungu wachilungamo ali kuti?’”