Malaki 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Inu mwanena kuti, ‘Kutumikira Mulungu nʼkopanda phindu.+ Tapindula chiyani chifukwa chomutumikira ndiponso chifukwa choyenda mwachisoni pamaso pa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba? Malaki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:14 Nsanja ya Olonda,2/15/2011, ptsa. 16-1712/15/2007, tsa. 297/1/1989, tsa. 30
14 “Inu mwanena kuti, ‘Kutumikira Mulungu nʼkopanda phindu.+ Tapindula chiyani chifukwa chomutumikira ndiponso chifukwa choyenda mwachisoni pamaso pa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba?