Mateyu 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 nʼkumuuza kuti: “Ngati ndinu mwana wa Mulungu mudziponye pansi, paja Malemba amati: ‘Iye adzalamula angelo ake zokhudza inu,’ komanso amati, ‘Adzakunyamulani mʼmanja mwawo, kuti phazi lanu lisawombe mwala.’”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:6 “Wotsatira Wanga,” ptsa. 60-61 Yesu—Ndi Njira, tsa. 36 Nsanja ya Olonda,5/15/2011, tsa. 18
6 nʼkumuuza kuti: “Ngati ndinu mwana wa Mulungu mudziponye pansi, paja Malemba amati: ‘Iye adzalamula angelo ake zokhudza inu,’ komanso amati, ‘Adzakunyamulani mʼmanja mwawo, kuti phazi lanu lisawombe mwala.’”+