Mateyu 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 n’kumuuza kuti: “Ngati ndinu mwana wa Mulungu, mudziponye pansi,+ pajatu Malemba amati, ‘Iye adzalamula angelo ake za inu, ndipo adzakunyamulani m’manja mwawo, kuti phazi lanu lisawombe mwala uliwonse.’”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:6 “Wotsatira Wanga,” ptsa. 60-61 Yesu—Ndi Njira, tsa. 36 Nsanja ya Olonda,5/15/2011, tsa. 18
6 n’kumuuza kuti: “Ngati ndinu mwana wa Mulungu, mudziponye pansi,+ pajatu Malemba amati, ‘Iye adzalamula angelo ake za inu, ndipo adzakunyamulani m’manja mwawo, kuti phazi lanu lisawombe mwala uliwonse.’”+