Mateyu 5:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense amene wathetsa ukwati ndi mkazi wake, osati chifukwa cha chiwerewere,* amachititsa kuti mkaziyo achite chigololo akakwatiwanso. Ndipo aliyense amene wakwatira mkazi wosiyidwayo nayenso wachita chigololo.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:32 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2018, ptsa. 11-12 Nsanja ya Olonda,8/15/1993, tsa. 510/1/1990, ptsa. 13, 15 Mtendere Weniweni, ptsa. 147-148
32 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense amene wathetsa ukwati ndi mkazi wake, osati chifukwa cha chiwerewere,* amachititsa kuti mkaziyo achite chigololo akakwatiwanso. Ndipo aliyense amene wakwatira mkazi wosiyidwayo nayenso wachita chigololo.+
5:32 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2018, ptsa. 11-12 Nsanja ya Olonda,8/15/1993, tsa. 510/1/1990, ptsa. 13, 15 Mtendere Weniweni, ptsa. 147-148