-
Mateyu 6:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Ndiye ngati Mulungu amaveka chonchi zomera zakutchire, zimene zimangokhalapo lero lokha mawa nʼkuzisonkheza pamoto, kodi iye sadzakuvekani kuposa pamenepo achikhulupiriro chochepa inu?
-