Mateyu 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nthawi inayake, pamene ankadya chakudya* mʼnyumba ina, kunabwera anthu ambiri okhometsa msonkho komanso ochimwa ndipo anayamba kudya* limodzi ndi Yesu ndi ophunzira ake.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:10 Yesu—Ndi Njira, tsa. 68 Nsanja ya Olonda,5/15/1986, ptsa. 8-9
10 Nthawi inayake, pamene ankadya chakudya* mʼnyumba ina, kunabwera anthu ambiri okhometsa msonkho komanso ochimwa ndipo anayamba kudya* limodzi ndi Yesu ndi ophunzira ake.+