Mateyu 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nthawi inayake, pamene anali kudya patebulo m’nyumba ina,+ kunabwera okhometsa msonkho ndi ochimwa ambiri ndipo anayamba kudya pamodzi ndi Yesu ndi ophunzira ake. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:10 Yesu—Ndi Njira, tsa. 68 Nsanja ya Olonda,5/15/1986, ptsa. 8-9
10 Nthawi inayake, pamene anali kudya patebulo m’nyumba ina,+ kunabwera okhometsa msonkho ndi ochimwa ambiri ndipo anayamba kudya pamodzi ndi Yesu ndi ophunzira ake.