Mateyu 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno mayi wina amene ankadwala matenda otaya magazi kwa zaka 12+ anafika kumbuyo kwake nʼkugwira ulusi wopota wamʼmphepete mwa malaya ake akunja,+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:20 Yesu—Ndi Njira, tsa. 116 Nsanja ya Olonda,7/15/1995, tsa. 166/1/1987, tsa. 24
20 Ndiyeno mayi wina amene ankadwala matenda otaya magazi kwa zaka 12+ anafika kumbuyo kwake nʼkugwira ulusi wopota wamʼmphepete mwa malaya ake akunja,+