Mateyu 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno atalowa mʼnyumba ya wolamulira uja, anaona anthu akuliza zitoliro komanso gulu la anthu likulira mofuula.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:23 Nsanja ya Olonda,2/1/2012, tsa. 14
23 Ndiyeno atalowa mʼnyumba ya wolamulira uja, anaona anthu akuliza zitoliro komanso gulu la anthu likulira mofuula.+