Mateyu 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano atalowa m’nyumba ya wolamulira uja,+ anaona oliza zitoliro komanso khamu la anthu likubuma.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:23 Nsanja ya Olonda,2/1/2012, tsa. 14
23 Tsopano atalowa m’nyumba ya wolamulira uja,+ anaona oliza zitoliro komanso khamu la anthu likubuma.+