Mateyu 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Choncho aliyense amene akuvomereza pamaso pa anthu kuti ndi wophunzira wanga,+ inenso ndidzamuvomereza pamaso pa Atate wanga wakumwamba kuti ndi wophunzira wanga.+
32 Choncho aliyense amene akuvomereza pamaso pa anthu kuti ndi wophunzira wanga,+ inenso ndidzamuvomereza pamaso pa Atate wanga wakumwamba kuti ndi wophunzira wanga.+