Mateyu 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “Chotero aliyense wovomereza pamaso pa anthu kuti ali kumbali yanga, inenso ndidzavomereza+ pamaso pa Atate wanga wakumwamba kuti ndili kumbali yake.
32 “Chotero aliyense wovomereza pamaso pa anthu kuti ali kumbali yanga, inenso ndidzavomereza+ pamaso pa Atate wanga wakumwamba kuti ndili kumbali yake.