Mateyu 10:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Aliyense amene akuyesa kupulumutsa moyo wake adzautaya, koma amene wataya moyo wake chifukwa cha ine adzaupeza.+
39 Aliyense amene akuyesa kupulumutsa moyo wake adzautaya, koma amene wataya moyo wake chifukwa cha ine adzaupeza.+