Mateyu 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Gulu lalikulu la anthu linasonkhana pamene iye anali, moti iye anakwera mʼngalawa nʼkukhala pansi, ndipo gulu lonse la anthulo linaimirira mʼmphepete mwa nyanjayo.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:2 Nsanja ya Olonda,6/15/1988, ptsa. 24-26
2 Gulu lalikulu la anthu linasonkhana pamene iye anali, moti iye anakwera mʼngalawa nʼkukhala pansi, ndipo gulu lonse la anthulo linaimirira mʼmphepete mwa nyanjayo.+