Mateyu 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mbewu zina zinagwera paminga ndipo mingazo zinakula nʼkulepheretsa mbewuzo kukula.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:7 Nsanja ya Olonda,2/1/2003, tsa. 12