Mateyu 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ulosi wa Yesaya ukukwaniritsidwa pa iwowa. Ulosiwo umanena kuti: ‘Kumva mudzamva ndithu, koma simudzazindikira tanthauzo lake. Kuyangʼana mudzangʼana ndithu, koma simudzaona chilichonse.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:14 Nsanja ya Olonda,4/1/1987, tsa. 8
14 Ulosi wa Yesaya ukukwaniritsidwa pa iwowa. Ulosiwo umanena kuti: ‘Kumva mudzamva ndithu, koma simudzazindikira tanthauzo lake. Kuyangʼana mudzangʼana ndithu, koma simudzaona chilichonse.+