Mateyu 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma chifukwa choti sakanakwanitsa kubweza ngongoleyo, mbuye wake analamula kuti mwamuna ameneyu, mkazi wake, ana ake komanso zonse zimene anali nazo zigulitsidwe nʼkumubwezera ndalama zake.+
25 Koma chifukwa choti sakanakwanitsa kubweza ngongoleyo, mbuye wake analamula kuti mwamuna ameneyu, mkazi wake, ana ake komanso zonse zimene anali nazo zigulitsidwe nʼkumubwezera ndalama zake.+