Mateyu 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma popeza kuti analibe choti apereke pobweza ngongoleyo, mbuye wake analamula kuti mwamuna ameneyu, mkazi wake, ana ake komanso zonse zimene anali nazo zigulitsidwe ndi kum’bwezera ndalama zake.+
25 Koma popeza kuti analibe choti apereke pobweza ngongoleyo, mbuye wake analamula kuti mwamuna ameneyu, mkazi wake, ana ake komanso zonse zimene anali nazo zigulitsidwe ndi kum’bwezera ndalama zake.+