Mateyu 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsoka kwa inu alembi ndi Afarisi, anthu achinyengo inu!+ Chifukwa mumawoloka nyanja komanso kuyenda mitunda italiitali kuti mukatembenuze munthu mmodzi. Koma akatembenuka mumamupangitsa kuti akhale woyenera kuponyedwa mʼGehena* kuposa inuyo. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:15 Nsanja ya Olonda,1/15/2008, tsa. 313/1/1992, tsa. 1310/1/1987, ptsa. 30-31
15 Tsoka kwa inu alembi ndi Afarisi, anthu achinyengo inu!+ Chifukwa mumawoloka nyanja komanso kuyenda mitunda italiitali kuti mukatembenuze munthu mmodzi. Koma akatembenuka mumamupangitsa kuti akhale woyenera kuponyedwa mʼGehena* kuposa inuyo.