Mateyu 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mofanana ndi zimenezi, pamaso pa anthu, inunso mumaoneka ngati olungama koma mkati mwanu mwadzaza chinyengo ndi kusamvera malamulo.+
28 Mofanana ndi zimenezi, pamaso pa anthu, inunso mumaoneka ngati olungama koma mkati mwanu mwadzaza chinyengo ndi kusamvera malamulo.+