Mateyu 23:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pa chifukwa chimenechi, ndikukutumizirani aneneri,+ anthu anzeru ndi aphunzitsi.+ Ena a iwo mudzawapha+ nʼkuwapachika pamtengo ndipo ena mudzawakwapula+ mʼmasunagoge mwanu ndi kuwazunza+ mumzinda ndi mzinda, Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:34 Yesu—Ndi Njira, tsa. 254 Nsanja ya Olonda,4/15/2013, ptsa. 12-13
34 Pa chifukwa chimenechi, ndikukutumizirani aneneri,+ anthu anzeru ndi aphunzitsi.+ Ena a iwo mudzawapha+ nʼkuwapachika pamtengo ndipo ena mudzawakwapula+ mʼmasunagoge mwanu ndi kuwazunza+ mumzinda ndi mzinda,