Mateyu 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako kunabwera kapolo amene analandira matalente awiri uja nʼkunena kuti, ‘Ambuye, paja munandipatsa matalente awiri koma taonani, ndapindula matalente enanso awiri.’+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:22 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2021, tsa. 22 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 262-263 Nsanja ya Olonda,6/15/1995, tsa. 17
22 Kenako kunabwera kapolo amene analandira matalente awiri uja nʼkunena kuti, ‘Ambuye, paja munandipatsa matalente awiri koma taonani, ndapindula matalente enanso awiri.’+
25:22 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2021, tsa. 22 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 262-263 Nsanja ya Olonda,6/15/1995, tsa. 17