-
Mateyu 25:43Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
43 Ndinali mlendo koma inu simunandilandire bwino. Ndinali wamaliseche koma inu simunandiveke. Ndinadwala komanso ndinali mʼndende koma inu simunandisamalire.’
-