Mateyu 25:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ndinali mlendo koma inu simunandilandire bwino. Ndinali wamaliseche koma inu simunandiveke.+ Ndinadwala komanso ndinali m’ndende,+ koma inu simunandisamalire.’
43 Ndinali mlendo koma inu simunandilandire bwino. Ndinali wamaliseche koma inu simunandiveke.+ Ndinadwala komanso ndinali m’ndende,+ koma inu simunandisamalire.’