Mateyu 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tsiku la Sabata litatha, mʼbandakucha wa tsiku loyamba la mlunguwo, Mariya wa ku Magadala ndi Mariya wina uja anabwera kudzaona manda.+
28 Tsiku la Sabata litatha, mʼbandakucha wa tsiku loyamba la mlunguwo, Mariya wa ku Magadala ndi Mariya wina uja anabwera kudzaona manda.+