Maliko 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako anachoka kumeneko nʼkufika mʼdera lakwawo+ ndipo ophunzira ake anamʼtsatira.