-
Maliko 6:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Koma anthu anawaona akuchoka ndipo ambiri anadziwa zimenezo. Choncho kuchokera mʼmizinda yonse anthu anathamangira kumeneko wapansi ndipo anthuwo ndi amene anayamba kukafika kumaloko.
-