Maliko 6:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma anthu anawaona akuchoka ndipo ambiri anadziwa zimenezo. Chotero kuchokera m’mizinda yonse, anthu anathamangira kumeneko wapansi, ndipo anthuwo ndi amene anayamba kukafika kumaloko.+
33 Koma anthu anawaona akuchoka ndipo ambiri anadziwa zimenezo. Chotero kuchokera m’mizinda yonse, anthu anathamangira kumeneko wapansi, ndipo anthuwo ndi amene anayamba kukafika kumaloko.+