Luka 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma khamu la anthu linadziwa ndi kum’tsatira. Iye anawalandirabe bwino ndi kuyamba kuwauza za ufumu wa Mulungu,+ ndipo anachiritsa amene anafunika kuchiritsidwa.+ Yohane 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma khamu lalikulu la anthu linali kumutsatira, chifukwa linali kuona zizindikiro zimene iye anali kuchita pa odwala.+
11 Koma khamu la anthu linadziwa ndi kum’tsatira. Iye anawalandirabe bwino ndi kuyamba kuwauza za ufumu wa Mulungu,+ ndipo anachiritsa amene anafunika kuchiritsidwa.+
2 Koma khamu lalikulu la anthu linali kumutsatira, chifukwa linali kuona zizindikiro zimene iye anali kuchita pa odwala.+