Maliko 6:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma anthu anawaona akuchoka ndipo ambiri anadziwa zimenezo. Chotero kuchokera m’mizinda yonse, anthu anathamangira kumeneko wapansi, ndipo anthuwo ndi amene anayamba kukafika kumaloko.+ Luka 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma khamu la anthu linadziwa ndi kum’tsatira. Iye anawalandirabe bwino ndi kuyamba kuwauza za ufumu wa Mulungu,+ ndipo anachiritsa amene anafunika kuchiritsidwa.+ Yohane 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano pamene anali mu Yerusalemu pa chikondwerero+ cha pasika, anthu ambiri anakhulupirira m’dzina lake,+ ataona zizindikiro zimene anali kuchita.+
33 Koma anthu anawaona akuchoka ndipo ambiri anadziwa zimenezo. Chotero kuchokera m’mizinda yonse, anthu anathamangira kumeneko wapansi, ndipo anthuwo ndi amene anayamba kukafika kumaloko.+
11 Koma khamu la anthu linadziwa ndi kum’tsatira. Iye anawalandirabe bwino ndi kuyamba kuwauza za ufumu wa Mulungu,+ ndipo anachiritsa amene anafunika kuchiritsidwa.+
23 Tsopano pamene anali mu Yerusalemu pa chikondwerero+ cha pasika, anthu ambiri anakhulupirira m’dzina lake,+ ataona zizindikiro zimene anali kuchita.+