Mateyu 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Yesu atatsika m’ngalawayo anaona khamu lalikulu la anthu, ndipo anawamvera chisoni,+ ndi kuwachiritsira anthu awo odwala.+ Maliko 6:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma potsika, anaona khamu lalikulu la anthu, ndipo anawamvera chifundo,+ chifukwa anali ngati nkhosa zopanda m’busa.+ Choncho anayamba kuwaphunzitsa zinthu zambiri.+ Yohane 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma khamu lalikulu la anthu linali kumutsatira, chifukwa linali kuona zizindikiro zimene iye anali kuchita pa odwala.+
14 Tsopano Yesu atatsika m’ngalawayo anaona khamu lalikulu la anthu, ndipo anawamvera chisoni,+ ndi kuwachiritsira anthu awo odwala.+
34 Koma potsika, anaona khamu lalikulu la anthu, ndipo anawamvera chifundo,+ chifukwa anali ngati nkhosa zopanda m’busa.+ Choncho anayamba kuwaphunzitsa zinthu zambiri.+
2 Koma khamu lalikulu la anthu linali kumutsatira, chifukwa linali kuona zizindikiro zimene iye anali kuchita pa odwala.+