Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 9:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Poona chikhamu cha anthu, iye anawamvera chisoni,+ chifukwa anali onyukanyuka ndi otayika ngati nkhosa zopanda m’busa.+

  • Mateyu 15:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Koma Yesu anaitana ophunzira ake n’kunena kuti:+ “Khamu la anthuli likundimvetsa chisoni,+ chifukwa anthuwa akhala ndi ine masiku atatu tsopano ndipo alibe chakudya. Sindikufuna kuwauza kuti azipita asanadye, chifukwa angalenguke panjira.”

  • Maliko 1:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Pamenepo anagwidwa chifundo,+ ndipo anatambasula dzanja lake n’kumukhudza. Kenako anamuuza kuti: “Ndikufuna. Khala woyera.”+

  • Luka 7:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pamene Ambuye anaona mayiwo, anawamvera chifundo,+ ndipo anawauza kuti: “Tontholani mayi.”+

  • Aheberi 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chotero, iye anayenera ndithu kukhala ngati “abale” ake m’zonse,+ kuti akhale mkulu wa ansembe wachifundo ndi wokhulupirika pa zinthu za Mulungu.+ Cholinga chake chinali choti apereke nsembe yophimba machimo+ kuti tikhalenso ogwirizana ndi Mulungu.+

  • Aheberi 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Amakhala woleza mtima pochita zinthu ndi anthu osadziwa kanthu ndi olakwa, chifukwa iyenso ndi wofooka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena