Luka 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma khamu la anthu linadziwa ndi kum’tsatira. Iye anawalandirabe bwino ndi kuyamba kuwauza za ufumu wa Mulungu,+ ndipo anachiritsa amene anafunika kuchiritsidwa.+
11 Koma khamu la anthu linadziwa ndi kum’tsatira. Iye anawalandirabe bwino ndi kuyamba kuwauza za ufumu wa Mulungu,+ ndipo anachiritsa amene anafunika kuchiritsidwa.+