Maliko 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo anati: “Mose analola kuti mwamuna azilemba kalata yothetsera ukwati nʼkusiya mkaziyo.”+