Maliko 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma Yesu anawauza kuti: “Chifukwa cha kuuma mtima kwanu+ iye anakulemberani lamulo limeneli.+