Maliko 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma Yesu anawauza kuti: “Iye anakulemberani lamulo limeneli chifukwa cha kuuma mtima kwanuku.+