-
Maliko 10:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 “Tsopano tikupita ku Yerusalemu ndipo Mwana wa munthu akaperekedwa kwa ansembe aakulu ndi alembi. Iwo akamuweruza kuti aphedwe ndipo akamupereka kwa anthu amitundu ina.
-