Maliko 10:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Tsopano kumene tikupitaku ndi ku Yerusalemu. Kumeneku Mwana wa munthu akaperekedwa kwa ansembe aakulu ndi alembi, ndipo akamuweruza kuti aphedwe, ndipo akam’pereka kwa anthu amitundu.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:33 Yesu—Ndi Njira, tsa. 228
33 “Tsopano kumene tikupitaku ndi ku Yerusalemu. Kumeneku Mwana wa munthu akaperekedwa kwa ansembe aakulu ndi alembi, ndipo akamuweruza kuti aphedwe, ndipo akam’pereka kwa anthu amitundu.+