Maliko 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mtundu udzaukirana ndi mtundu wina ndipo ufumu udzaukirana ndi ufumu wina.+ Kudzakhala zivomerezi mʼmalo osiyanasiyana ndiponso kudzakhala njala.+ Zimenezi ndi chiyambi cha mavuto aakulu.*+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:8 Nsanja ya Olonda,5/1/2011, tsa. 53/15/2008, tsa. 1210/15/1988, tsa. 3
8 Mtundu udzaukirana ndi mtundu wina ndipo ufumu udzaukirana ndi ufumu wina.+ Kudzakhala zivomerezi mʼmalo osiyanasiyana ndiponso kudzakhala njala.+ Zimenezi ndi chiyambi cha mavuto aakulu.*+