Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 24:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mtundu udzaukirana ndi mtundu wina ndipo ufumu udzaukirana ndi ufumu wina.+ Kudzakhala njala+ ndi zivomerezi mʼmalo osiyanasiyana.+

  • Luka 21:10, 11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kenako anawauza kuti: “Mtundu udzaukirana ndi mtundu wina+ ndipo ufumu udzaukirana ndi ufumu wina.+ 11 Kudzachitika zivomerezi zamphamvu ndipo kudzakhala miliri+ ndi njala mʼmalo osiyanasiyana. Kudzaoneka zinthu zoopsa ndipo kumwamba kudzaoneka zizindikiro zodabwitsa.

  • Chivumbulutso 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kenako ndinamva ngati wina akulankhula kuchokera pakati pa angelo 4 aja kuti: “Kilogalamu imodzi* ya tirigu, mtengo wake ukhala dinari* imodzi,+ ndipo makilogalamu atatu a balere, mtengo wake ukhala dinari imodzi. Koma musawononge mafuta a maolivi ndi vinyo.”+

  • Chivumbulutso 6:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Nditayangʼana, ndinaona hatchi yotuwa. Amene anakwera pahatchiyi dzina lake anali Imfa. Ndipo Manda* ankamutsatira pafupi kwambiri. Iwo anapatsidwa ulamuliro pa gawo limodzi la magawo 4 adziko lapansi, kuti aphe anthu ndi lupanga lalitali, njala,+ mliri woopsa komanso zilombo zapadziko lapansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena